×

Iwo ali ngati amene adadza pambuyo pawo amene adalandira dipo loipa chifukwa 59:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:15) ayat 15 in Chichewa

59:15 Surah Al-hashr ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 15 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿كَمَثَلِ ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِهِمۡ قَرِيبٗاۖ ذَاقُواْ وَبَالَ أَمۡرِهِمۡ وَلَهُمۡ عَذَابٌ أَلِيمٞ ﴾
[الحَشر: 15]

Iwo ali ngati amene adadza pambuyo pawo amene adalandira dipo loipa chifukwa cha ntchito zawo ndipo iwo adzalandira chilango chowawa kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: كمثل الذين من قبلهم قريبا ذاقوا وبال أمرهم ولهم عذاب أليم, باللغة نيانجا

﴿كمثل الذين من قبلهم قريبا ذاقوا وبال أمرهم ولهم عذاب أليم﴾ [الحَشر: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Fanizo (la Ayuda a Banu Nadhiri) lili ngati (amene adatsutsa mwa Ayuda a Qainuka) amene awatsogolera (kupeza mavuto) posachedwapa, adalawa chilango (pa dziko lapansi) cha zochita zawo (ndi kuswa mapangano). Ndipo iwo adzalandira chilango (china) chowawa kwambiri, (pa tsiku la chiweruziro)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek