×

Iwo sadzamenyana nawe ngati gulu limodzi ayi koma mozemba pogwiritsa ntchito Malinga 59:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:14) ayat 14 in Chichewa

59:14 Surah Al-hashr ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 14 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿لَا يُقَٰتِلُونَكُمۡ جَمِيعًا إِلَّا فِي قُرٗى مُّحَصَّنَةٍ أَوۡ مِن وَرَآءِ جُدُرِۭۚ بَأۡسُهُم بَيۡنَهُمۡ شَدِيدٞۚ تَحۡسَبُهُمۡ جَمِيعٗا وَقُلُوبُهُمۡ شَتَّىٰۚ ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمۡ قَوۡمٞ لَّا يَعۡقِلُونَ ﴾
[الحَشر: 14]

Iwo sadzamenyana nawe ngati gulu limodzi ayi koma mozemba pogwiritsa ntchito Malinga ya m’mizinda kapena pobisala kuzipupa. Mtima womenya nkhondo ulipo pakati pawo moti iwe ukhoza kuganiza kuti ndi ogwirizana. Koma mitima yawo ndi yogawikana chifukwa iwo ndi anthu osadziwa chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لا يقاتلونكم جميعا إلا في قرى محصنة أو من وراء جدر بأسهم, باللغة نيانجا

﴿لا يقاتلونكم جميعا إلا في قرى محصنة أو من وراء جدر بأسهم﴾ [الحَشر: 14]

Khaled Ibrahim Betala
“(Ayuda) sangamenyane ndi inu ali pa gulu kupatula m’midzi yotetezedwa ndi malinga, kapena kuseri kwa zipupa. Nkhondo yawo pakati pawo njaukali; ungawaganizire kuti ali pamodzi pomwe mitima yawo njosiyana; zimenezo nchifukwa chakuti iwo ndianthu opanda nzeru
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek