Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 16 - الحَشر - Page - Juz 28
﴿كَمَثَلِ ٱلشَّيۡطَٰنِ إِذۡ قَالَ لِلۡإِنسَٰنِ ٱكۡفُرۡ فَلَمَّا كَفَرَ قَالَ إِنِّي بَرِيٓءٞ مِّنكَ إِنِّيٓ أَخَافُ ٱللَّهَ رَبَّ ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[الحَشر: 16]
﴿كمثل الشيطان إذ قال للإنسان اكفر فلما كفر قال إني بريء منك﴾ [الحَشر: 16]
Khaled Ibrahim Betala “Fanizo la achinyengo (achiphamaso pakuwanyenga Banu Nadhiri kuti amupandukire Mneneri wa Allah) lili ngati satana (ponyenga munthu kusiya chikhulupiliro). Adati kwa Iye: “Mkane (Allah).” Ndipo pamene adamkana, (satana) adati: “Ine sindili ndi iwe; ndithu ine ndikuopa Allah, Mbuye wa zolengedwa.” |