×

Ndipo inu musakhale ngati iwo amene adaiwala Mulungu ndipo Iye adawachititsa kuti 59:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:19) ayat 19 in Chichewa

59:19 Surah Al-hashr ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 19 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿وَلَا تَكُونُواْ كَٱلَّذِينَ نَسُواْ ٱللَّهَ فَأَنسَىٰهُمۡ أَنفُسَهُمۡۚ أُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡفَٰسِقُونَ ﴾
[الحَشر: 19]

Ndipo inu musakhale ngati iwo amene adaiwala Mulungu ndipo Iye adawachititsa kuti adziiwale eni ake. Amenewa ndiwo amene amaphwanya malamulo mopitiriza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تكونوا كالذين نسوا الله فأنساهم أنفسهم أولئك هم الفاسقون, باللغة نيانجا

﴿ولا تكونوا كالذين نسوا الله فأنساهم أنفسهم أولئك هم الفاسقون﴾ [الحَشر: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo musakhale monga amene aiwala (zoyenera kuchitira) Allah; choncho (naye Allah) wawaiwalitsa mitima yawo (powachotsera kuzindikira zimene zingawathandize). Amenewa ndiwo olakwa kwakukulu (otuluka ku chilamulo cha Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek