×

oh inu anthu okhulupirira! opani Mulungu. Ndipo kwaniritsani udindo wanu kwa Iye. 59:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:18) ayat 18 in Chichewa

59:18 Surah Al-hashr ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 18 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ ٱتَّقُواْ ٱللَّهَ وَلۡتَنظُرۡ نَفۡسٞ مَّا قَدَّمَتۡ لِغَدٖۖ وَٱتَّقُواْ ٱللَّهَۚ إِنَّ ٱللَّهَ خَبِيرُۢ بِمَا تَعۡمَلُونَ ﴾
[الحَشر: 18]

oh inu anthu okhulupirira! opani Mulungu. Ndipo kwaniritsani udindo wanu kwa Iye. Ndipo ulekeni mzimu uliwonse uganize zimene udzalandire mawa ndipo opani Mulungu. Ndithudi Mulungu amadziwa chilichonse chimene mumachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا اتقوا الله ولتنظر نفس ما قدمت لغد واتقوا الله, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا اتقوا الله ولتنظر نفس ما قدمت لغد واتقوا الله﴾ [الحَشر: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Muopeni Allah (potsatira malamulo Ake ndi kusiya zimene waletsa) ndipo alingalire munthu aliyense zamawa zimene watsogoza. Ndipo muopeni Allah, ndithu Allah Ngodziwa zimene mukuchita (ndipo adzakulipirani pa zimenezo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek