Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 164 - الأنعَام - Page - Juz 8
﴿قُلۡ أَغَيۡرَ ٱللَّهِ أَبۡغِي رَبّٗا وَهُوَ رَبُّ كُلِّ شَيۡءٖۚ وَلَا تَكۡسِبُ كُلُّ نَفۡسٍ إِلَّا عَلَيۡهَاۚ وَلَا تَزِرُ وَازِرَةٞ وِزۡرَ أُخۡرَىٰۚ ثُمَّ إِلَىٰ رَبِّكُم مَّرۡجِعُكُمۡ فَيُنَبِّئُكُم بِمَا كُنتُمۡ فِيهِ تَخۡتَلِفُونَ ﴾
[الأنعَام: 164]
﴿قل أغير الله أبغي ربا وهو رب كل شيء ولا تكسب كل﴾ [الأنعَام: 164]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Kodi ndifune mbuye wina kusiya Allah, pomwe Iye ndi Mbuye wa chinthu chilichonse? Ndipo mzimu uliwonse siuchita choipa koma ukudzichitira wokha. Mzimu wosenza machimo siudzasenza machimo a mzimu wina. Kenako kobwerera kwanu (nonse) ndi kwa Mbuye wanu, (Allah), ndipo adzakuuzani zomwe mudali kusiyana.” |