×

Ndipo usawathamangitse iwo amene amapembedza Ambuye wawo m’mawa ndi madzulo pofuna chisangalalo 6:52 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:52) ayat 52 in Chichewa

6:52 Surah Al-An‘am ayat 52 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 52 - الأنعَام - Page - Juz 7

﴿وَلَا تَطۡرُدِ ٱلَّذِينَ يَدۡعُونَ رَبَّهُم بِٱلۡغَدَوٰةِ وَٱلۡعَشِيِّ يُرِيدُونَ وَجۡهَهُۥۖ مَا عَلَيۡكَ مِنۡ حِسَابِهِم مِّن شَيۡءٖ وَمَا مِنۡ حِسَابِكَ عَلَيۡهِم مِّن شَيۡءٖ فَتَطۡرُدَهُمۡ فَتَكُونَ مِنَ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الأنعَام: 52]

Ndipo usawathamangitse iwo amene amapembedza Ambuye wawo m’mawa ndi madzulo pofuna chisangalalo chake. Iwe siudzaimbidwa mlandu pa zochita zawo ndipo nawonso sadzaimbidwa mlandu pa zochita zako ndipo ngati iwe uwathamangitsa udzakhala mugulu la anthu opanda chilungamo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تطرد الذين يدعون ربهم بالغداة والعشي يريدون وجهه ما عليك من, باللغة نيانجا

﴿ولا تطرد الذين يدعون ربهم بالغداة والعشي يريدون وجهه ما عليك من﴾ [الأنعَام: 52]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek