Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 54 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿وَإِذَا جَآءَكَ ٱلَّذِينَ يُؤۡمِنُونَ بِـَٔايَٰتِنَا فَقُلۡ سَلَٰمٌ عَلَيۡكُمۡۖ كَتَبَ رَبُّكُمۡ عَلَىٰ نَفۡسِهِ ٱلرَّحۡمَةَ أَنَّهُۥ مَنۡ عَمِلَ مِنكُمۡ سُوٓءَۢا بِجَهَٰلَةٖ ثُمَّ تَابَ مِنۢ بَعۡدِهِۦ وَأَصۡلَحَ فَأَنَّهُۥ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[الأنعَام: 54]
﴿وإذا جاءك الذين يؤمنون بآياتنا فقل سلام عليكم كتب ربكم على نفسه﴾ [الأنعَام: 54]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (iwe Mneneri) akakudzera (awo osauka) amene akhulupirira zizindikiro zathu (atalakwa pang’ono), auze: “Mtendere ukhale pa inu. Mbuye wanu wadzikakamiza kukhala Wachifundo, kuti mwa inu amene achite choipa mwaumbuli, koma pambuyo pake nkulapa, nachita zabwino, Allah amkhululukira; Iye Ngokhululuka kwambiri, Ngwachisoni chosatha.” |