Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 69 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿وَمَا عَلَى ٱلَّذِينَ يَتَّقُونَ مِنۡ حِسَابِهِم مِّن شَيۡءٖ وَلَٰكِن ذِكۡرَىٰ لَعَلَّهُمۡ يَتَّقُونَ ﴾
[الأنعَام: 69]
﴿وما على الذين يتقون من حسابهم من شيء ولكن ذكرى لعلهم يتقون﴾ [الأنعَام: 69]
Khaled Ibrahim Betala “Palibe chilichonse chimene chingawapeze oopa Allah chochokera m’chiwerengero cha oipawo, koma chofunika kwa iwo (oopa Allah) ndikuwakumbutsa (oipawo) kuti aope (aleke zomwe akunenazo) |