Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 97 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿وَهُوَ ٱلَّذِي جَعَلَ لَكُمُ ٱلنُّجُومَ لِتَهۡتَدُواْ بِهَا فِي ظُلُمَٰتِ ٱلۡبَرِّ وَٱلۡبَحۡرِۗ قَدۡ فَصَّلۡنَا ٱلۡأٓيَٰتِ لِقَوۡمٖ يَعۡلَمُونَ ﴾
[الأنعَام: 97]
﴿وهو الذي جعل لكم النجوم لتهتدوا بها في ظلمات البر والبحر قد﴾ [الأنعَام: 97]
Khaled Ibrahim Betala “Iye ndi amene anakupangirani nyenyezi kuti mulondole njira kudzera mwa izo mu m’dima wa pamtunda ndi panyanja. Ndithu talongosola mokwanira zizindikiro (zathu) kwa anthu odziwa |