×

“Ambuye wathu, musatisandutse ife kukhala mayesero a anthu osakhulupirira koma tikhululukireni Ambuye 60:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mumtahanah ⮕ (60:5) ayat 5 in Chichewa

60:5 Surah Al-Mumtahanah ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mumtahanah ayat 5 - المُمتَحنَة - Page - Juz 28

﴿رَبَّنَا لَا تَجۡعَلۡنَا فِتۡنَةٗ لِّلَّذِينَ كَفَرُواْ وَٱغۡفِرۡ لَنَا رَبَّنَآۖ إِنَّكَ أَنتَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[المُمتَحنَة: 5]

“Ambuye wathu, musatisandutse ife kukhala mayesero a anthu osakhulupirira koma tikhululukireni Ambuye wathu. Ndithudi Inu ndinu Mwini mphamvu zonse ndi Mwini nzeru zonse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ربنا لا تجعلنا فتنة للذين كفروا واغفر لنا ربنا إنك أنت العزيز, باللغة نيانجا

﴿ربنا لا تجعلنا فتنة للذين كفروا واغفر لنا ربنا إنك أنت العزيز﴾ [المُمتَحنَة: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“E Mbuye wathu! Musatichite kukhala mayeso kwa amene sadakhulupirire, tikhululukireni Mbuye wathu! Ndithu Inu, Ndinu Amphamvu zopambana ndiponso Anzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek