×

Mulungu wakuletsani kuchita ubwenzi ndi anthu amene munamenyana nawo chifukwa cha chikhulupiriro 60:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mumtahanah ⮕ (60:9) ayat 9 in Chichewa

60:9 Surah Al-Mumtahanah ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mumtahanah ayat 9 - المُمتَحنَة - Page - Juz 28

﴿إِنَّمَا يَنۡهَىٰكُمُ ٱللَّهُ عَنِ ٱلَّذِينَ قَٰتَلُوكُمۡ فِي ٱلدِّينِ وَأَخۡرَجُوكُم مِّن دِيَٰرِكُمۡ وَظَٰهَرُواْ عَلَىٰٓ إِخۡرَاجِكُمۡ أَن تَوَلَّوۡهُمۡۚ وَمَن يَتَوَلَّهُمۡ فَأُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلظَّٰلِمُونَ ﴾
[المُمتَحنَة: 9]

Mulungu wakuletsani kuchita ubwenzi ndi anthu amene munamenyana nawo chifukwa cha chikhulupiriro ndipo anakuthamangitsani ku nyumba zanu kapena adathandiza anthu ena kuti amenyane ndi kukupirikitsani inu. Ndipo aliyense amene achita ubwenzi ndi anthu otere ndi ochimwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنما ينهاكم الله عن الذين قاتلوكم في الدين وأخرجوكم من دياركم وظاهروا, باللغة نيانجا

﴿إنما ينهاكم الله عن الذين قاتلوكم في الدين وأخرجوكم من دياركم وظاهروا﴾ [المُمتَحنَة: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah akukuletsani kugwirizana nawo amene adakumenyani chifukwa cha chipembedzo ndi kukutulutsani m’nyumba zanu, ndi amene adathandiza kukutulutsani. Amene ati agwirizane nawo iwowo ndiwo achinyengo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek