×

Ndi pamene Mose adanena ndi anthu ake: “oh inu anthu anga! Kodi 61:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-saff ⮕ (61:5) ayat 5 in Chichewa

61:5 Surah As-saff ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-saff ayat 5 - الصَّف - Page - Juz 28

﴿وَإِذۡ قَالَ مُوسَىٰ لِقَوۡمِهِۦ يَٰقَوۡمِ لِمَ تُؤۡذُونَنِي وَقَد تَّعۡلَمُونَ أَنِّي رَسُولُ ٱللَّهِ إِلَيۡكُمۡۖ فَلَمَّا زَاغُوٓاْ أَزَاغَ ٱللَّهُ قُلُوبَهُمۡۚ وَٱللَّهُ لَا يَهۡدِي ٱلۡقَوۡمَ ٱلۡفَٰسِقِينَ ﴾
[الصَّف: 5]

Ndi pamene Mose adanena ndi anthu ake: “oh inu anthu anga! Kodi bwanji mukundikwiyitsa pamene muli kudziwa kuti ine ndine Mtumwi wa Mulungu kwa inuyo?” Ndipo pamene iwo adalakwa, Mulungu adalola kuti mitima yawo ilakwe. Ndipo Mulungu satsogolera anthu ophwanya malamulo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ قال موسى لقومه ياقوم لم تؤذونني وقد تعلمون أني رسول الله, باللغة نيانجا

﴿وإذ قال موسى لقومه ياقوم لم تؤذونني وقد تعلمون أني رسول الله﴾ [الصَّف: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kumbuka (iwe Mneneri{s.a.w}) pamene Mûsa adanena kwa anthu ake kuti: “Ndichifukwa ninji mukundivutitsa ine pomwe mukudziwa kuti ine ndine Mtumiki wa Allah kwa inu?” Ndipo pamene adapitiriza kupandukira choonadi, Allah adaipinda mitima yawo (kuti isalandire chiongoko); ndipo Allah saongola anthu otuluka m’chilamulo Chake
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek