×

Nena: “Ndithudi imfa imene muli kuopa, ndithudi, idzadza pa inu ndipo inu 62:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jumu‘ah ⮕ (62:8) ayat 8 in Chichewa

62:8 Surah Al-Jumu‘ah ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jumu‘ah ayat 8 - الجُمعَة - Page - Juz 28

﴿قُلۡ إِنَّ ٱلۡمَوۡتَ ٱلَّذِي تَفِرُّونَ مِنۡهُ فَإِنَّهُۥ مُلَٰقِيكُمۡۖ ثُمَّ تُرَدُّونَ إِلَىٰ عَٰلِمِ ٱلۡغَيۡبِ وَٱلشَّهَٰدَةِ فَيُنَبِّئُكُم بِمَا كُنتُمۡ تَعۡمَلُونَ ﴾
[الجُمعَة: 8]

Nena: “Ndithudi imfa imene muli kuopa, ndithudi, idzadza pa inu ndipo inu mudzabwerera kwa Iye amene amadziwa zinthu zonse zobisika ndi zooneka ndipo Iye adzakuuzani zonse zimene munali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل إن الموت الذي تفرون منه فإنه ملاقيكم ثم تردون إلى عالم, باللغة نيانجا

﴿قل إن الموت الذي تفرون منه فإنه ملاقيكم ثم تردون إلى عالم﴾ [الجُمعَة: 8]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena (kuti): “Ndithu imfa imene mukuithawa (palibe chipeneko) ikumana nanu; kenako muzabwezedwa kwa wodziwa zobisika ndi zooneka; ndipo adzakuuzani zimene mudali kuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek