×

Oh inu anthu okhulupirira! Ngati mumva kuitana kwa mapemphero a masana a 62:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jumu‘ah ⮕ (62:9) ayat 9 in Chichewa

62:9 Surah Al-Jumu‘ah ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jumu‘ah ayat 9 - الجُمعَة - Page - Juz 28

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِذَا نُودِيَ لِلصَّلَوٰةِ مِن يَوۡمِ ٱلۡجُمُعَةِ فَٱسۡعَوۡاْ إِلَىٰ ذِكۡرِ ٱللَّهِ وَذَرُواْ ٱلۡبَيۡعَۚ ذَٰلِكُمۡ خَيۡرٞ لَّكُمۡ إِن كُنتُمۡ تَعۡلَمُونَ ﴾
[الجُمعَة: 9]

Oh inu anthu okhulupirira! Ngati mumva kuitana kwa mapemphero a masana a tsiku lachisanu, fulumirani kukakumbukira Mulungu ndipo siyani ntchito zanu. Chimenechondichochabwinokwainungatimukadadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا إذا نودي للصلاة من يوم الجمعة فاسعوا إلى ذكر, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا إذا نودي للصلاة من يوم الجمعة فاسعوا إلى ذكر﴾ [الجُمعَة: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Kukaitanidwa ku Swala (pemphero la Ijuma) tsiku la Ijuma, pitani mwachangu kukamtamanda Allah. Ndipo siyani malonda; zimenezo (mwalamulidwazo) nzabwino kwa inu ngati mukudziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek