×

Palibe vuto limene limadza popanda chilolezo cha Mulungu ndipo aliyense amene amakhulupirira 64:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taghabun ⮕ (64:11) ayat 11 in Chichewa

64:11 Surah At-Taghabun ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taghabun ayat 11 - التغَابُن - Page - Juz 28

﴿مَآ أَصَابَ مِن مُّصِيبَةٍ إِلَّا بِإِذۡنِ ٱللَّهِۗ وَمَن يُؤۡمِنۢ بِٱللَّهِ يَهۡدِ قَلۡبَهُۥۚ وَٱللَّهُ بِكُلِّ شَيۡءٍ عَلِيمٞ ﴾
[التغَابُن: 11]

Palibe vuto limene limadza popanda chilolezo cha Mulungu ndipo aliyense amene amakhulupirira mwa Mulungu, Iye amatsogolera mtima wake ndipo Mulungu amadziwa chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما أصاب من مصيبة إلا بإذن الله ومن يؤمن بالله يهد قلبه, باللغة نيانجا

﴿ما أصاب من مصيبة إلا بإذن الله ومن يؤمن بالله يهد قلبه﴾ [التغَابُن: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Palibe vuto lililonse lingapezeke pokhapokha Allah atafuna; ndipo amene akhulupirira Allah, (Allah) aongola mtima wake (kuti ukhale wokhutira ndi chiweruzo cha Allah). Ndipo Allah Ngodziwa chinthu chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek