×

Ngati mukongoza Mulungu ngongole yabwino, Iye adzaichulukitsa ndipo adzakukhululukirani machimo anu. Ndipo 64:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taghabun ⮕ (64:17) ayat 17 in Chichewa

64:17 Surah At-Taghabun ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taghabun ayat 17 - التغَابُن - Page - Juz 28

﴿إِن تُقۡرِضُواْ ٱللَّهَ قَرۡضًا حَسَنٗا يُضَٰعِفۡهُ لَكُمۡ وَيَغۡفِرۡ لَكُمۡۚ وَٱللَّهُ شَكُورٌ حَلِيمٌ ﴾
[التغَابُن: 17]

Ngati mukongoza Mulungu ngongole yabwino, Iye adzaichulukitsa ndipo adzakukhululukirani machimo anu. Ndipo Mulungu ndi wokonzeka kuyamika ndi kulipira ndipo ndi wopilira kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن تقرضوا الله قرضا حسنا يضاعفه لكم ويغفر لكم والله شكور حليم, باللغة نيانجا

﴿إن تقرضوا الله قرضا حسنا يضاعفه لكم ويغفر لكم والله شكور حليم﴾ [التغَابُن: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati mungamkongoze Allah ngongole yabwino aiwonjezera kwa inu (malipiro ake) ndipo akukhululukirani (zolakwa zanu.) Ndipo Allah Ngolandira kuthokoza, Ngoleza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek