×

Ngati inu awiri mulapa machimo anu kwa Mulungu ndipo mitima yanu itsimikiza 66:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Tahrim ⮕ (66:4) ayat 4 in Chichewa

66:4 Surah At-Tahrim ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Tahrim ayat 4 - التَّحرِيم - Page - Juz 28

﴿إِن تَتُوبَآ إِلَى ٱللَّهِ فَقَدۡ صَغَتۡ قُلُوبُكُمَاۖ وَإِن تَظَٰهَرَا عَلَيۡهِ فَإِنَّ ٱللَّهَ هُوَ مَوۡلَىٰهُ وَجِبۡرِيلُ وَصَٰلِحُ ٱلۡمُؤۡمِنِينَۖ وَٱلۡمَلَٰٓئِكَةُ بَعۡدَ ذَٰلِكَ ظَهِيرٌ ﴾
[التَّحرِيم: 4]

Ngati inu awiri mulapa machimo anu kwa Mulungu ndipo mitima yanu itsimikiza kutero, koma ngati inu mugwirizana kulimbana naye, ndithudi, Mulungu ndiye Mtetezi wake, ndi Gabriele ndipo aliyense wolungama amene ali pakati pa anthu amene akhulupirira ndi angelo. Onse ndi omuthandiza iye

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن تتوبا إلى الله فقد صغت قلوبكما وإن تظاهرا عليه فإن الله, باللغة نيانجا

﴿إن تتوبا إلى الله فقد صغت قلوبكما وإن تظاهرا عليه فإن الله﴾ [التَّحرِيم: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati awirinu mulapa kwa Allah pazimene mwachita (chitani changu kulapa) chifukwa chakuti mitima yanu yapotoka pang’ono (chifukwa cha nsanje pa zimene Mneneri akufuna zosunga chinsinsi Chake); koma ngati awirinu muthandizana pazimene zingamvutitse, ndithu Allah ndiye Mtetezi wake ndi Jibril (Gabriele) ndiponso okhulupirira abwino; naonso angelo, kuonjezera apa ndiathandizi (ake)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek