×

Zingatheke kuti pamene iye akusudzulani inu, Mulungu adzamupatsa m’malo mwanu, akazi ena 66:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Tahrim ⮕ (66:5) ayat 5 in Chichewa

66:5 Surah At-Tahrim ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Tahrim ayat 5 - التَّحرِيم - Page - Juz 28

﴿عَسَىٰ رَبُّهُۥٓ إِن طَلَّقَكُنَّ أَن يُبۡدِلَهُۥٓ أَزۡوَٰجًا خَيۡرٗا مِّنكُنَّ مُسۡلِمَٰتٖ مُّؤۡمِنَٰتٖ قَٰنِتَٰتٖ تَٰٓئِبَٰتٍ عَٰبِدَٰتٖ سَٰٓئِحَٰتٖ ثَيِّبَٰتٖ وَأَبۡكَارٗا ﴾
[التَّحرِيم: 5]

Zingatheke kuti pamene iye akusudzulani inu, Mulungu adzamupatsa m’malo mwanu, akazi ena abwino oposa inu amene amadzipereka kwa Mulungu, amene ali okhulupirira, opirira, olapa kwa Mulungu, opembedza modzichepetsa, osala zifuniro zawo, kapena obwera amene anakwatiwapo kale kapena a namwali

❮ Previous Next ❯

ترجمة: عسى ربه إن طلقكن أن يبدله أزواجا خيرا منكن مسلمات مؤمنات قانتات, باللغة نيانجا

﴿عسى ربه إن طلقكن أن يبدله أزواجا خيرا منكن مسلمات مؤمنات قانتات﴾ [التَّحرِيم: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati (Mtumiki) akakusudzulani, ndithu Mbuye wake, ampatsa akazi ena mmalo mwa inu, abwino kuposa inu: ogonjera (Allah), okhulupirira (ndi mitima yawo), omvera, olapa, odzichepetsa (pamaso pa Allah) ochita mapemphero (kwambiri), oyenda (pa chikhulupiliro cha Allah kapena ochulukitsa kusala) amene adakwatiwapo kale ndi osakwatiwapo.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek