Quran with Chichewa translation - Surah At-Tahrim ayat 6 - التَّحرِيم - Page - Juz 28
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ قُوٓاْ أَنفُسَكُمۡ وَأَهۡلِيكُمۡ نَارٗا وَقُودُهَا ٱلنَّاسُ وَٱلۡحِجَارَةُ عَلَيۡهَا مَلَٰٓئِكَةٌ غِلَاظٞ شِدَادٞ لَّا يَعۡصُونَ ٱللَّهَ مَآ أَمَرَهُمۡ وَيَفۡعَلُونَ مَا يُؤۡمَرُونَ ﴾
[التَّحرِيم: 6]
﴿ياأيها الذين آمنوا قوا أنفسكم وأهليكم نارا وقودها الناس والحجارة عليها ملائكة﴾ [التَّحرِيم: 6]
Khaled Ibrahim Betala “E inu amene mwakhulupirira! Dzitchinjirizeni inu ndi mawanja anu ku Moto umene nkhuni zake ndi anthu ndi miyala; oyang’anira ake ndi angelo ouma mtima, amphamvu, sanyoza Allah pa zimene Wawalamula, ndipo amachita (zokhazo) zimene alamulidwa |