Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 100 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿أَوَلَمۡ يَهۡدِ لِلَّذِينَ يَرِثُونَ ٱلۡأَرۡضَ مِنۢ بَعۡدِ أَهۡلِهَآ أَن لَّوۡ نَشَآءُ أَصَبۡنَٰهُم بِذُنُوبِهِمۡۚ وَنَطۡبَعُ عَلَىٰ قُلُوبِهِمۡ فَهُمۡ لَا يَسۡمَعُونَ ﴾
[الأعرَاف: 100]
﴿أو لم يهد للذين يرثون الأرض من بعد أهلها أن لو نشاء﴾ [الأعرَاف: 100]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi sadadziwe awa omwe alandira dziko molowa mmalo pambuyo pa eni dzikolo (anthu akale) kuti tikadafuna tikadawaika m’masautso chifukwa cha machimo awo ndi kuwadinda mitima yawo kotero iwo sakadamva (kanthu) |