×

Mulungu adati: “Kodi chakuletsa ndi chiyani kuti umugwadire iye pamene Ine nditakulamula 7:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:12) ayat 12 in Chichewa

7:12 Surah Al-A‘raf ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 12 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿قَالَ مَا مَنَعَكَ أَلَّا تَسۡجُدَ إِذۡ أَمَرۡتُكَۖ قَالَ أَنَا۠ خَيۡرٞ مِّنۡهُ خَلَقۡتَنِي مِن نَّارٖ وَخَلَقۡتَهُۥ مِن طِينٖ ﴾
[الأعرَاف: 12]

Mulungu adati: “Kodi chakuletsa ndi chiyani kuti umugwadire iye pamene Ine nditakulamula kutero?” Iye adati: “Ine ndine wolemekezeka kuposa Adamu. Inu mudandilenga ine kuchokera ku moto pamene iye mudamulenga kuchokera ku dothi.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال ما منعك ألا تسجد إذ أمرتك قال أنا خير منه خلقتني, باللغة نيانجا

﴿قال ما منعك ألا تسجد إذ أمرتك قال أنا خير منه خلقتني﴾ [الأعرَاف: 12]

Khaled Ibrahim Betala
“(Allah) adati: “Nchiyani chakuletsa kumgwadira pamene ndakulamula?” (Satana) anati: “Ine ndine wabwino kuposa iye. Ine munandilenga ndi moto koma iye mudamulenga ndi dongo.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek