×

Ndipo anthu ake a Mose adaumba, iye atachoka, kuchokera ku mphete ndi 7:148 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:148) ayat 148 in Chichewa

7:148 Surah Al-A‘raf ayat 148 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 148 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَٱتَّخَذَ قَوۡمُ مُوسَىٰ مِنۢ بَعۡدِهِۦ مِنۡ حُلِيِّهِمۡ عِجۡلٗا جَسَدٗا لَّهُۥ خُوَارٌۚ أَلَمۡ يَرَوۡاْ أَنَّهُۥ لَا يُكَلِّمُهُمۡ وَلَا يَهۡدِيهِمۡ سَبِيلًاۘ ٱتَّخَذُوهُ وَكَانُواْ ظَٰلِمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 148]

Ndipo anthu ake a Mose adaumba, iye atachoka, kuchokera ku mphete ndi ndolo zawo, chifanizo cha mwana wa ng’ombe amene adali ndi mawu. Kodi iwo sadathe kuona kuti iyo siinathe kuwalankhula kapena kuwalondolera njira? Iwo adaipembedza iyo, kotero adalakwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واتخذ قوم موسى من بعده من حليهم عجلا جسدا له خوار ألم, باللغة نيانجا

﴿واتخذ قوم موسى من بعده من حليهم عجلا جسدا له خوار ألم﴾ [الأعرَاف: 148]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pambuyo pake (popita kukalandira Taurat), anthu a Mûsa adaumba (fano la) thole (mwana wa ng’ombe) kuchokera mu zodzikongoletsera zawo (zibangiri zawo za siliva ndi golide); yemwe adali ndi thupi ndi kumatuluka mawu (koma wopanda moyo). Kodi sakuona kuti ilo (fano lawolo) silikuwalankhula ndiponso silikuwaongolera njira (yabwino?) Koma adalipanga basi (kuti likhale mulungu wawo wa fano) potero adali kudzichitira okha zoipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek