×

Iwo amene akana zizindikiro zathu ndi kukumana kwa patsiku la chiweruzo ntchito 7:147 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:147) ayat 147 in Chichewa

7:147 Surah Al-A‘raf ayat 147 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 147 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَٱلَّذِينَ كَذَّبُواْ بِـَٔايَٰتِنَا وَلِقَآءِ ٱلۡأٓخِرَةِ حَبِطَتۡ أَعۡمَٰلُهُمۡۚ هَلۡ يُجۡزَوۡنَ إِلَّا مَا كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[الأعرَاف: 147]

Iwo amene akana zizindikiro zathu ndi kukumana kwa patsiku la chiweruzo ntchito zawo ndi zopanda pake. Kodi iwo amayembekeza kuti adzalipidwa kuposa zimene amachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين كذبوا بآياتنا ولقاء الآخرة حبطت أعمالهم هل يجزون إلا ما كانوا, باللغة نيانجا

﴿والذين كذبوا بآياتنا ولقاء الآخرة حبطت أعمالهم هل يجزون إلا ما كانوا﴾ [الأعرَاف: 147]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo awo amene atsutsa zizindikiro Zathu ndi nkumano wa tsiku lachimaliziro, zochita zawo zaonongeka. Kodi adzalipidwa china kuposa zomwe adali kuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek