×

Koma pamene iwo adazindikira ndi kuona kuti adalakwa, iwo adati: “Ngati Ambuye 7:149 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:149) ayat 149 in Chichewa

7:149 Surah Al-A‘raf ayat 149 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 149 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَلَمَّا سُقِطَ فِيٓ أَيۡدِيهِمۡ وَرَأَوۡاْ أَنَّهُمۡ قَدۡ ضَلُّواْ قَالُواْ لَئِن لَّمۡ يَرۡحَمۡنَا رَبُّنَا وَيَغۡفِرۡ لَنَا لَنَكُونَنَّ مِنَ ٱلۡخَٰسِرِينَ ﴾
[الأعرَاف: 149]

Koma pamene iwo adazindikira ndi kuona kuti adalakwa, iwo adati: “Ngati Ambuye wathu sakhala ndi chifundo ndi ife ndi kutikhululukira, ndithudi, ife tidzakhala anthu otayika.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولما سقط في أيديهم ورأوا أنهم قد ضلوا قالوا لئن لم يرحمنا, باللغة نيانجا

﴿ولما سقط في أيديهم ورأوا أنهم قد ضلوا قالوا لئن لم يرحمنا﴾ [الأعرَاف: 149]

Khaled Ibrahim Betala
“Pamene adazindikira kulakwa kwawo, (anadandaula kwambiri) naona kuti iwo asokera, anati: “Ngati Mbuye wathu satimvera chisoni ndi kutikhululukira, ndithudi, tikhala mwa otaika (oonongeka).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek