×

Koma iwo amene anachita zoipa ndipo pambuyo pake adalapa ndi kukhala ndi 7:153 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:153) ayat 153 in Chichewa

7:153 Surah Al-A‘raf ayat 153 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 153 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَٱلَّذِينَ عَمِلُواْ ٱلسَّيِّـَٔاتِ ثُمَّ تَابُواْ مِنۢ بَعۡدِهَا وَءَامَنُوٓاْ إِنَّ رَبَّكَ مِنۢ بَعۡدِهَا لَغَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[الأعرَاف: 153]

Koma iwo amene anachita zoipa ndipo pambuyo pake adalapa ndi kukhala ndi chikhulupiriro, ndithu Ambuye wako pambuyo pa izo ndi wokhululukira ndi wachisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين عملوا السيئات ثم تابوا من بعدها وآمنوا إن ربك من بعدها, باللغة نيانجا

﴿والذين عملوا السيئات ثم تابوا من بعدها وآمنوا إن ربك من بعدها﴾ [الأعرَاف: 153]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo omwe adachita zoipa, kenako nkulapa pambuyo pake nakhulupirira ndithu Mbuye wako pambuyo pakulapako, Ngokhululuka kwabasi, Ngwachisoni
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek