Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 191 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿أَيُشۡرِكُونَ مَا لَا يَخۡلُقُ شَيۡـٔٗا وَهُمۡ يُخۡلَقُونَ ﴾ 
[الأعرَاف: 191]
﴿أيشركون ما لا يخلق شيئا وهم يخلقون﴾ [الأعرَاف: 191]
| Khaled Ibrahim Betala “Kodi akumphatikiza (Allah) ndi zinthu zomwe sizilenga chilichonse pomwe izo zikulengedwa |