Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 2 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿كِتَٰبٌ أُنزِلَ إِلَيۡكَ فَلَا يَكُن فِي صَدۡرِكَ حَرَجٞ مِّنۡهُ لِتُنذِرَ بِهِۦ وَذِكۡرَىٰ لِلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[الأعرَاف: 2]
﴿كتاب أنـزل إليك فلا يكن في صدرك حرج منه لتنذر به وذكرى﴾ [الأعرَاف: 2]
Khaled Ibrahim Betala “(Iyi Qur’an ndi) buku (lopatulika) lomwe lavumbulutsidwa kwa iwe. Choncho chifuwa chako chisabanike ndi ilo (poopa kufikitsa mawu ake kwa anthu kuti angakuyese wabodza;) kuti uwachenjeze nalo (otsutsa) ndi kuti likhale chikumbutso kwa okhulupirira (kuti aonjezere chikhulupiliro chawo) |