×

Ndipo Satana anawanong’oneza iwo onse ndi cholinga choti chionekere kwa iwo chimene 7:20 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:20) ayat 20 in Chichewa

7:20 Surah Al-A‘raf ayat 20 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 20 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿فَوَسۡوَسَ لَهُمَا ٱلشَّيۡطَٰنُ لِيُبۡدِيَ لَهُمَا مَا وُۥرِيَ عَنۡهُمَا مِن سَوۡءَٰتِهِمَا وَقَالَ مَا نَهَىٰكُمَا رَبُّكُمَا عَنۡ هَٰذِهِ ٱلشَّجَرَةِ إِلَّآ أَن تَكُونَا مَلَكَيۡنِ أَوۡ تَكُونَا مِنَ ٱلۡخَٰلِدِينَ ﴾
[الأعرَاف: 20]

Ndipo Satana anawanong’oneza iwo onse ndi cholinga choti chionekere kwa iwo chimene chinali chobisika ndi chochititsa manyazi ndipo Satana adati: “Ambuye wanu adakuletsani kuti musayandikire mtengo uwu chifukwa sadafune kuti mukhale angelo kapena anthu a muyaya.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فوسوس لهما الشيطان ليبدي لهما ما ووري عنهما من سوآتهما وقال ما, باللغة نيانجا

﴿فوسوس لهما الشيطان ليبدي لهما ما ووري عنهما من سوآتهما وقال ما﴾ [الأعرَاف: 20]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho satana adawanong’oneza (zoipa) kuti awaonetsere zomwe zidabisika kwa iwo za maliseche awo. Ndipo (satana) adati: “Mbuye wanu sadakuletseni mtengo uwu, koma pachifukwa chakuti mungasanduke angelo awiri, kapena kuti mungakhale okhala nthawi yaitali.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek