×

“O iwe Adamu! Khala iwe ndi mkazi wako ku Paradiso ndipo idyani 7:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:19) ayat 19 in Chichewa

7:19 Surah Al-A‘raf ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 19 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿وَيَٰٓـَٔادَمُ ٱسۡكُنۡ أَنتَ وَزَوۡجُكَ ٱلۡجَنَّةَ فَكُلَا مِنۡ حَيۡثُ شِئۡتُمَا وَلَا تَقۡرَبَا هَٰذِهِ ٱلشَّجَرَةَ فَتَكُونَا مِنَ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 19]

“O iwe Adamu! Khala iwe ndi mkazi wako ku Paradiso ndipo idyani mmenemo monga mungafunire, koma inu musadzayandikire mtengo uwu chifukwa nonse mungadzakhale odzipondereza nokha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وياآدم اسكن أنت وزوجك الجنة فكلا من حيث شئتما ولا تقربا هذه, باللغة نيانجا

﴿وياآدم اسكن أنت وزوجك الجنة فكلا من حيث شئتما ولا تقربا هذه﴾ [الأعرَاف: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kenako Allah adanena kwa Adam) “E iwe Adam! Khala ndi mkazi wako m’Munda wamtendere (sangalalani ndi zomwe zili m’menemo), idyani paliponse pamene mwafuna. Koma mtego uwu musawuyandikire kuopera kuti mungakhale m’gulu la odzichitira okha zoipa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek