Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 21 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿وَقَاسَمَهُمَآ إِنِّي لَكُمَا لَمِنَ ٱلنَّٰصِحِينَ ﴾
[الأعرَاف: 21]
﴿وقاسمهما إني لكما لمن الناصحين﴾ [الأعرَاف: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adawalumbilira onse awiri kuti: “Ndithudi, ine ndine mmodzi mwa olangiza (ndikukufunirani zabwino).” |