×

Ndipo kumbukira Ambuye wako ndi lilime lako, mwa iwe wekha, modzichepetsa ndi 7:205 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:205) ayat 205 in Chichewa

7:205 Surah Al-A‘raf ayat 205 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 205 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَٱذۡكُر رَّبَّكَ فِي نَفۡسِكَ تَضَرُّعٗا وَخِيفَةٗ وَدُونَ ٱلۡجَهۡرِ مِنَ ٱلۡقَوۡلِ بِٱلۡغُدُوِّ وَٱلۡأٓصَالِ وَلَا تَكُن مِّنَ ٱلۡغَٰفِلِينَ ﴾
[الأعرَاف: 205]

Ndipo kumbukira Ambuye wako ndi lilime lako, mwa iwe wekha, modzichepetsa ndi mwamantha ndiponso mosakweza mawu m’mawa ndi masana ndipo usakhale ngati iwo a unyizi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واذكر ربك في نفسك تضرعا وخيفة ودون الجهر من القول بالغدو والآصال, باللغة نيانجا

﴿واذكر ربك في نفسك تضرعا وخيفة ودون الجهر من القول بالغدو والآصال﴾ [الأعرَاف: 205]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mtchule Mbuye wako mu mtima mwako modzichepetsa, mwa mantha ndi mosakweza mawu m’mawa ndi madzulo; ndipo usakhale mwa osalabadila (malamulo a Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek