×

Gulu lina adalitsogolera ndipo gulu lina liyenera kusochera chifukwa, ndithudi, iwo adasankha 7:30 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:30) ayat 30 in Chichewa

7:30 Surah Al-A‘raf ayat 30 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 30 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿فَرِيقًا هَدَىٰ وَفَرِيقًا حَقَّ عَلَيۡهِمُ ٱلضَّلَٰلَةُۚ إِنَّهُمُ ٱتَّخَذُواْ ٱلشَّيَٰطِينَ أَوۡلِيَآءَ مِن دُونِ ٱللَّهِ وَيَحۡسَبُونَ أَنَّهُم مُّهۡتَدُونَ ﴾
[الأعرَاف: 30]

Gulu lina adalitsogolera ndipo gulu lina liyenera kusochera chifukwa, ndithudi, iwo adasankha a Satana kuti akhale owathandiza ndi atetezi awo m’malo mwa Mulungu ndipo anali kuganizira kuti adali otsogolera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فريقا هدى وفريقا حق عليهم الضلالة إنهم اتخذوا الشياطين أولياء من دون, باللغة نيانجا

﴿فريقا هدى وفريقا حق عليهم الضلالة إنهم اتخذوا الشياطين أولياء من دون﴾ [الأعرَاف: 30]

Khaled Ibrahim Betala
“Gulu lina waliongola, pomwe gulu lina patsimikizika pa ilo kusokera chifukwa chakuti iwo adasankha asatana kukhala atetezi (awo) kusiya Allah; ndipo akuganiza kuti iwo ngoongoka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek