×

Nena, “Ambuye wanga walamula chilungamo ndi kuti muzimupembedza Iye yekha. Mpembedzeni Iye. 7:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:29) ayat 29 in Chichewa

7:29 Surah Al-A‘raf ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 29 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿قُلۡ أَمَرَ رَبِّي بِٱلۡقِسۡطِۖ وَأَقِيمُواْ وُجُوهَكُمۡ عِندَ كُلِّ مَسۡجِدٖ وَٱدۡعُوهُ مُخۡلِصِينَ لَهُ ٱلدِّينَۚ كَمَا بَدَأَكُمۡ تَعُودُونَ ﴾
[الأعرَاف: 29]

Nena, “Ambuye wanga walamula chilungamo ndi kuti muzimupembedza Iye yekha. Mpembedzeni Iye. Monga momwe adakulengerani poyamba kwa Iye mudzabwerera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل أمر ربي بالقسط وأقيموا وجوهكم عند كل مسجد وادعوه مخلصين له, باللغة نيانجا

﴿قل أمر ربي بالقسط وأقيموا وجوهكم عند كل مسجد وادعوه مخلصين له﴾ [الأعرَاف: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Mbuye wanga walamula chilungamo; ndiponso (wandiuza kuti ndikuuzeni kuti) lungamitsani nkhope zanu (kwa Iye) m’nthawi ya Swala iliyonse, ndipo mpembedzeni Iye Yekha momuyeretsera chipembedzo monga Iye adakulengani pachiyambi, momwemonso mudzabwerera kwa Iye.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek