×

Ndipo mizinda ndi yambiri imene Ife tidaononga! Chilango chathu chidadza pa iwo 7:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:4) ayat 4 in Chichewa

7:4 Surah Al-A‘raf ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 4 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿وَكَم مِّن قَرۡيَةٍ أَهۡلَكۡنَٰهَا فَجَآءَهَا بَأۡسُنَا بَيَٰتًا أَوۡ هُمۡ قَآئِلُونَ ﴾
[الأعرَاف: 4]

Ndipo mizinda ndi yambiri imene Ife tidaononga! Chilango chathu chidadza pa iwo usiku kapena pamene iwo adali kugona nthawi ya masana

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكم من قرية أهلكناها فجاءها بأسنا بياتا أو هم قائلون, باللغة نيانجا

﴿وكم من قرية أهلكناها فجاءها بأسنا بياتا أو هم قائلون﴾ [الأعرَاف: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndimidzi yambiri imene tidaiononga ndipo chilango Chathu chidaidzera nthawi ya usiku, kapena usana iwo atagona tulo tamasana (akupumula monga momwe zinawachitikira anthu a Loti ndi anthu a Shuaib)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek