×

Iwo sadalire mwa mtundu wina uli wonse pamene chilango chathu chinadza kupatula 7:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:5) ayat 5 in Chichewa

7:5 Surah Al-A‘raf ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 5 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿فَمَا كَانَ دَعۡوَىٰهُمۡ إِذۡ جَآءَهُم بَأۡسُنَآ إِلَّآ أَن قَالُوٓاْ إِنَّا كُنَّا ظَٰلِمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 5]

Iwo sadalire mwa mtundu wina uli wonse pamene chilango chathu chinadza kupatula kuti: “Ndithudi ife tidali anthu olakwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فما كان دعواهم إذ جاءهم بأسنا إلا أن قالوا إنا كنا ظالمين, باللغة نيانجا

﴿فما كان دعواهم إذ جاءهم بأسنا إلا أن قالوا إنا كنا ظالمين﴾ [الأعرَاف: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo sikunali kulira kwawo pamene chinawafika chilango chathu koma kunena (ndi kuvomereza): “Ndithudi, ife tinali ochita zoipa.” (Koma kuvomereza kwawoko sikunawapindulire kanthu)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek