Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 44 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿وَنَادَىٰٓ أَصۡحَٰبُ ٱلۡجَنَّةِ أَصۡحَٰبَ ٱلنَّارِ أَن قَدۡ وَجَدۡنَا مَا وَعَدَنَا رَبُّنَا حَقّٗا فَهَلۡ وَجَدتُّم مَّا وَعَدَ رَبُّكُمۡ حَقّٗاۖ قَالُواْ نَعَمۡۚ فَأَذَّنَ مُؤَذِّنُۢ بَيۡنَهُمۡ أَن لَّعۡنَةُ ٱللَّهِ عَلَى ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 44]
﴿ونادى أصحاب الجنة أصحاب النار أن قد وجدنا ما وعدنا ربنا حقا﴾ [الأعرَاف: 44]
Khaled Ibrahim Betala “Anthu a ku Munda wamtendere adzaitana anthu aku Moto (adzanena kuti): “Ndithudi ife tapeza zimene Mbuye wathu adatilonjeza kuti nzoona. Kodi nanunso mwapeza zomwe Mbuye wanu adakulonjezani kuti nzoona?” (Anthu a ku Moto) adzanena: “Inde.” Choncho wolengeza pakati pawo adzalengeza kuti: “Matembelero a Allah ali pa anthu ochita zoipa.” |