×

Ndipo anthu a m’chipupa adzawaitana anthu omwe adzawadziwa ndi zizindikiro zawo ndipo 7:48 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:48) ayat 48 in Chichewa

7:48 Surah Al-A‘raf ayat 48 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 48 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿وَنَادَىٰٓ أَصۡحَٰبُ ٱلۡأَعۡرَافِ رِجَالٗا يَعۡرِفُونَهُم بِسِيمَىٰهُمۡ قَالُواْ مَآ أَغۡنَىٰ عَنكُمۡ جَمۡعُكُمۡ وَمَا كُنتُمۡ تَسۡتَكۡبِرُونَ ﴾
[الأعرَاف: 48]

Ndipo anthu a m’chipupa adzawaitana anthu omwe adzawadziwa ndi zizindikiro zawo ndipo adzati: “Kodi kuchuluka kwanu, kwakuthandizani chiani ndiponso mwano umene mumaonetsa ku chipembedzo?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ونادى أصحاب الأعراف رجالا يعرفونهم بسيماهم قالوا ما أغنى عنكم جمعكم وما, باللغة نيانجا

﴿ونادى أصحاب الأعراف رجالا يعرفونهم بسيماهم قالوا ما أغنى عنكم جمعكم وما﴾ [الأعرَاف: 48]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo anthu aja apachikweza adzawaitana anthu (a ku Moto), adzawadziwa ndi zizindikiro zawo, nati: “Sikudakuthandizeni kuchuluka kwanu kuja, ngakhale zija mudali kudzitama nazo.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek