Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 7 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿فَلَنَقُصَّنَّ عَلَيۡهِم بِعِلۡمٖۖ وَمَا كُنَّا غَآئِبِينَ ﴾
[الأعرَاف: 7]
﴿فلنقصن عليهم بعلم وما كنا غائبين﴾ [الأعرَاف: 7]
Khaled Ibrahim Betala “Tsono tidzawauza mozindikira bwino-bwino (chilichonse chimene ankachita). Ndipo sitidali kutali (nawo pamene ankachita zochita zawo) |