Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 95 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿ثُمَّ بَدَّلۡنَا مَكَانَ ٱلسَّيِّئَةِ ٱلۡحَسَنَةَ حَتَّىٰ عَفَواْ وَّقَالُواْ قَدۡ مَسَّ ءَابَآءَنَا ٱلضَّرَّآءُ وَٱلسَّرَّآءُ فَأَخَذۡنَٰهُم بَغۡتَةٗ وَهُمۡ لَا يَشۡعُرُونَ ﴾
[الأعرَاف: 95]
﴿ثم بدلنا مكان السيئة الحسنة حتى عفوا وقالوا قد مس آباءنا الضراء﴾ [الأعرَاف: 95]
Khaled Ibrahim Betala “Kenako tinasintha pamalo pa choipa pobweretsapo chabwino, (tidawachotsera masautso ndi mavuto ngakhale sadali okhulupirira) mpaka anachuluka, ndi kuchulukanso chuma chawo; anayamba kunena kuti: “Masautso ndi mavuto adawakhudzaponso makolo athu. (Zoterezi sizachilendo kwa ife).” Choncho tidawaononga mwadzidzidzi asakudziwa |