×

Tsiku limene adzatuluka mwansanga m’manda mwawo ngati anthu a pa mpikisano umene 70:43 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma‘arij ⮕ (70:43) ayat 43 in Chichewa

70:43 Surah Al-Ma‘arij ayat 43 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma‘arij ayat 43 - المَعَارج - Page - Juz 29

﴿يَوۡمَ يَخۡرُجُونَ مِنَ ٱلۡأَجۡدَاثِ سِرَاعٗا كَأَنَّهُمۡ إِلَىٰ نُصُبٖ يُوفِضُونَ ﴾
[المَعَارج: 43]

Tsiku limene adzatuluka mwansanga m’manda mwawo ngati anthu a pa mpikisano umene amalandirirapo mphotho

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يوم يخرجون من الأجداث سراعا كأنهم إلى نصب يوفضون, باللغة نيانجا

﴿يوم يخرجون من الأجداث سراعا كأنهم إلى نصب يوفضون﴾ [المَعَارج: 43]

Khaled Ibrahim Betala
“Tsiku limene adzatuluke m’manda uku akuthamanga (kudza kwa woitana) ngati kuti akuthamangira kumafano awo (amene adali kuwapembedza)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek