Quran with Chichewa translation - Surah Nuh ayat 14 - نُوح - Page - Juz 29
﴿وَقَدۡ خَلَقَكُمۡ أَطۡوَارًا ﴾
[نُوح: 14]
﴿وقد خلقكم أطوارا﴾ [نُوح: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Pomwe Iye adakulengani mnjira zosiyanasiyana; (madzi a umunthu, kenako magazi, kenako magazi ochindikala, kenako mafupa ndipo kenako mnofu) |