Quran with Chichewa translation - Surah Nuh ayat 2 - نُوح - Page - Juz 29
﴿قَالَ يَٰقَوۡمِ إِنِّي لَكُمۡ نَذِيرٞ مُّبِينٌ ﴾
[نُوح: 2]
﴿قال ياقوم إني لكم نذير مبين﴾ [نُوح: 2]
Khaled Ibrahim Betala “Adanena (Nuh): “E inu anthu anga! Ndithu ine ndimchenjezi kwa inu woonekera poyera (wolongosola za uthenga wa Mbuye wanu m’chiyankhulo chimene mukuchidziwa).” |