Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 10 - الجِن - Page - Juz 29
﴿وَأَنَّا لَا نَدۡرِيٓ أَشَرٌّ أُرِيدَ بِمَن فِي ٱلۡأَرۡضِ أَمۡ أَرَادَ بِهِمۡ رَبُّهُمۡ رَشَدٗا ﴾
[الجِن: 10]
﴿وأنا لا ندري أشر أريد بمن في الأرض أم أراد بهم ربهم﴾ [الجِن: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu ife sitikudziwa chilango chimene akuwafunira a m’dziko (polondera kumwamba, kuletsa kumvetsera nkhani zakumeneko); kapena Mbuye wawo akuwafunira zabwino ndi chilungamo (pa zimenezo) |