Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 9 - الجِن - Page - Juz 29
﴿وَأَنَّا كُنَّا نَقۡعُدُ مِنۡهَا مَقَٰعِدَ لِلسَّمۡعِۖ فَمَن يَسۡتَمِعِ ٱلۡأٓنَ يَجِدۡ لَهُۥ شِهَابٗا رَّصَدٗا ﴾
[الجِن: 9]
﴿وأنا كنا نقعد منها مقاعد للسمع فمن يستمع الآن يجد له شهابا﴾ [الجِن: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu ife tidali kukhala m’menemo (kale) mokhala momvetsera; (mobera nkhani zakumwamba). Koma amene afune kumvetsera tsopano apeza chenje cha moto chikudikilira (kuti chimgwere iye ndi kumuononga) |