Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 23 - الجِن - Page - Juz 29
﴿إِلَّا بَلَٰغٗا مِّنَ ٱللَّهِ وَرِسَٰلَٰتِهِۦۚ وَمَن يَعۡصِ ٱللَّهَ وَرَسُولَهُۥ فَإِنَّ لَهُۥ نَارَ جَهَنَّمَ خَٰلِدِينَ فِيهَآ أَبَدًا ﴾
[الجِن: 23]
﴿إلا بلاغا من الله ورسالاته ومن يعص الله ورسوله فإن له نار﴾ [الجِن: 23]
Khaled Ibrahim Betala ““Koma (mphamvu imene ndili nayo) ndikufikitsa uthenga wa Allah umene adanditumizira; ndithu amene anyoza Allah ndi Mtumiki Wake (ndi kupatuka pa chipembedzo cha (Allah) ndithu moto wa Jahannam ndi wake, akakhala m’menemo muyaya.” |