Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 27 - الجِن - Page - Juz 29
﴿إِلَّا مَنِ ٱرۡتَضَىٰ مِن رَّسُولٖ فَإِنَّهُۥ يَسۡلُكُ مِنۢ بَيۡنِ يَدَيۡهِ وَمِنۡ خَلۡفِهِۦ رَصَدٗا ﴾
[الجِن: 27]
﴿إلا من ارتضى من رسول فإنه يسلك من بين يديه ومن خلفه﴾ [الجِن: 27]
Khaled Ibrahim Betala ““Kupatula Mtumiki (Wake) amene wamuyanja; (iyeyo amamdziwitsa zobisikazo) ndipo ndithu amamuikira alonda kutsogolo kwake ndi kumbuyo kwake (omulonda).” |