Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qiyamah ayat 2 - القِيَامة - Page - Juz 29
﴿وَلَآ أُقۡسِمُ بِٱلنَّفۡسِ ٱللَّوَّامَةِ ﴾ 
[القِيَامة: 2]
﴿ولا أقسم بالنفس اللوامة﴾ [القِيَامة: 2]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndikulumbiliranso mzimu wodzidzudzula (pa cholakwa chimene wachita. Ndithu mudzaukitsidwa; mafupa anu omwazikana atasonkhanitsidwa) |