×

Ndifeamenetidawalengandipo tinaika mphamvu m’ziwalo zawo. Koma ngati Ife titafuna, tikhoza kulenga anthu 76:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Insan ⮕ (76:28) ayat 28 in Chichewa

76:28 Surah Al-Insan ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 28 - الإنسَان - Page - Juz 29

﴿نَّحۡنُ خَلَقۡنَٰهُمۡ وَشَدَدۡنَآ أَسۡرَهُمۡۖ وَإِذَا شِئۡنَا بَدَّلۡنَآ أَمۡثَٰلَهُمۡ تَبۡدِيلًا ﴾
[الإنسَان: 28]

Ndifeamenetidawalengandipo tinaika mphamvu m’ziwalo zawo. Koma ngati Ife titafuna, tikhoza kulenga anthu ena kuti alowe m’malo mwawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: نحن خلقناهم وشددنا أسرهم وإذا شئنا بدلنا أمثالهم تبديلا, باللغة نيانجا

﴿نحن خلقناهم وشددنا أسرهم وإذا شئنا بدلنا أمثالهم تبديلا﴾ [الإنسَان: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“Ife ndi amene tidawalenga ndipo tidalimbika kalengedwe kawo; ndipo titafuna tingabweretse ena onga iwo (omvera Allah) kulowa m’malo mwawo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek