Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 6 - الإنسَان - Page - Juz 29
﴿عَيۡنٗا يَشۡرَبُ بِهَا عِبَادُ ٱللَّهِ يُفَجِّرُونَهَا تَفۡجِيرٗا ﴾
[الإنسَان: 6]
﴿عينا يشرب بها عباد الله يفجرونها تفجيرا﴾ [الإنسَان: 6]
Khaled Ibrahim Betala “(Kaafura ameneyo) ndikasupe amene adzikamwapo akapolo a Allah ndi kumtulutsa (paliponse pamene afuna) kumtulutsa mofewa |